Numeri 31:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 chilichonse chimene sichingapse ndi moto, chidutse pamoto kuti chikhale choyera. Kenako muzichiyeretsanso ndi madzi.+ Koma chilichonse chimene chingapse ndi moto muzichiyeretsa ndi madzi.
23 chilichonse chimene sichingapse ndi moto, chidutse pamoto kuti chikhale choyera. Kenako muzichiyeretsanso ndi madzi.+ Koma chilichonse chimene chingapse ndi moto muzichiyeretsa ndi madzi.