Numeri 31:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pa hafu imene Aisiraeli alandira, mutengepo chamoyo chimodzi pa zamoyo 50 zilizonse, pa anthu, ngʼombe, abulu, nkhosa ndi pa ziweto zamtundu uliwonse. Muzipereke kwa Alevi,+ amene amagwira ntchito zokhudzana ndi utumiki wapachihema cha Yehova.”+
30 Pa hafu imene Aisiraeli alandira, mutengepo chamoyo chimodzi pa zamoyo 50 zilizonse, pa anthu, ngʼombe, abulu, nkhosa ndi pa ziweto zamtundu uliwonse. Muzipereke kwa Alevi,+ amene amagwira ntchito zokhudzana ndi utumiki wapachihema cha Yehova.”+