Numeri 31:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Kenako atsogoleri a masauzande a asilikali+ anafika kwa Mose. Iwowa anali atsogoleri a magulu a asilikali 1,000 ndi atsogoleri a magulu a asilikali 100.
48 Kenako atsogoleri a masauzande a asilikali+ anafika kwa Mose. Iwowa anali atsogoleri a magulu a asilikali 1,000 ndi atsogoleri a magulu a asilikali 100.