Numeri 31:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Iwo anauza Mose kuti: “Ife atumiki anu tawerenga amuna onse ankhondo amene tikuwayangʼanira, ndipo palibe ndi mmodzi yemwe amene akusowapo.+
49 Iwo anauza Mose kuti: “Ife atumiki anu tawerenga amuna onse ankhondo amene tikuwayangʼanira, ndipo palibe ndi mmodzi yemwe amene akusowapo.+