Numeri 31:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Golide yense amene anamupereka kwa Yehova anakwana masekeli* 16,750. Ameneyu ndi golide amene atsogoleri a magulu a asilikali 1,000 komanso atsogoleri a magulu a asilikali 100 anapereka.
52 Golide yense amene anamupereka kwa Yehova anakwana masekeli* 16,750. Ameneyu ndi golide amene atsogoleri a magulu a asilikali 1,000 komanso atsogoleri a magulu a asilikali 100 anapereka.