-
Numeri 31:54Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
54 Choncho Mose ndi wansembe Eleazara analandira zinthu zagolidezo kwa atsogoleri a magulu a asilikali 1,000, ndiponso kwa atsogoleri a magulu a asilikali 100. Ndipo zinthu zagolidezo anakaziika mʼchihema chokumanako, kuti zikhale chikumbutso kwa Aisiraeli pamaso pa Yehova.
-