Numeri 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndi madera amene Yehova anawagonjetsa kuti akhale a Aisiraeli.+ Madera amenewa ndi abwino kwa ziweto, ndipo atumiki anufe tili ndi ziweto zambiri.”+
4 ndi madera amene Yehova anawagonjetsa kuti akhale a Aisiraeli.+ Madera amenewa ndi abwino kwa ziweto, ndipo atumiki anufe tili ndi ziweto zambiri.”+