Numeri 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ndiponso mpaka dzikolo litagonjetsedwa pamaso pa Yehova.+ Pambuyo pake mukhoza kudzabwerera+ ndipo mudzakhala opanda mlandu kwa Yehova ndi kwa Isiraeli. Kenako dzikoli lidzakhala lanu pamaso pa Yehova.+
22 ndiponso mpaka dzikolo litagonjetsedwa pamaso pa Yehova.+ Pambuyo pake mukhoza kudzabwerera+ ndipo mudzakhala opanda mlandu kwa Yehova ndi kwa Isiraeli. Kenako dzikoli lidzakhala lanu pamaso pa Yehova.+