-
Numeri 32:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Koma mukapanda kuchita zimenezi, mudzakhala kuti mwachimwira Yehova. Ndipo mukatero, dziwani kuti tchimo lanu lidzakutsatani.
-