Numeri 32:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma atumiki anufe tiwoloka, aliyense atatenga zida kukamenya nkhondo pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zimene mwanena mbuyathu.”
27 Koma atumiki anufe tiwoloka, aliyense atatenga zida kukamenya nkhondo pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zimene mwanena mbuyathu.”