-
Numeri 32:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Choncho Mose anapereka lamulo lokhudza iwowo kwa wansembe Eleazara, Yoswa mwana wa Nuni ndi kwa atsogoleri a mafuko a Isiraeli.
-