Numeri 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye anawauza kuti: “Ngati ana a Gadi ndi ana a Rubeni atawoloka nanu Yorodano, aliyense atatenga zida kuti akamenye nkhondo pamaso pa Yehova, nʼkugonjetsa dzikolo pamaso panu, mudzawapatse dziko la Giliyadi kuti likhale cholowa chawo.+
29 Iye anawauza kuti: “Ngati ana a Gadi ndi ana a Rubeni atawoloka nanu Yorodano, aliyense atatenga zida kuti akamenye nkhondo pamaso pa Yehova, nʼkugonjetsa dzikolo pamaso panu, mudzawapatse dziko la Giliyadi kuti likhale cholowa chawo.+