Numeri 33:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atanyamuka ku Alusi, anakamanga msasa ku Refidimu,+ kumene kunalibe madzi oti anthu amwe.