Numeri 34:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Malirewo adzakhota nʼkukadutsa kumʼmwera kwa chitunda cha Akirabimu+ kulowera ku Zini, nʼkukathera kumʼmwera kwa Kadesi-barinea.+ Kenako akakhotere ku Hazara-adara+ nʼkukafika ku Azimoni.
4 Malirewo adzakhota nʼkukadutsa kumʼmwera kwa chitunda cha Akirabimu+ kulowera ku Zini, nʼkukathera kumʼmwera kwa Kadesi-barinea.+ Kenako akakhotere ku Hazara-adara+ nʼkukafika ku Azimoni.