Numeri 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Malire anu akumpoto akayende motere: Mukalembe malirewo kuchokera ku Nyanja Yaikulu mpaka kuphiri la Hora.+
7 Malire anu akumpoto akayende motere: Mukalembe malirewo kuchokera ku Nyanja Yaikulu mpaka kuphiri la Hora.+