Numeri 34:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amenewa ndi amuna amene Yehova anawalamula kuti akagawe malo kwa Aisiraeli mʼdziko la Kanani.+