-
Numeri 35:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ngati wagenda mnzake ndi mwala woti ungaphe munthu, mnzakeyo nʼkufa, ameneyo ndi wopha munthu. Ndipo wopha munthuyo aphedwe ndithu.
-