-
Numeri 35:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 kapena ngati samamuona ndipo wamugwetsera mwala, mnzakeyo nʼkufa, koma sanali mdani wake komanso analibe cholinga choti amuvulaze,
-