Numeri 35:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kenako oweruzawo azipulumutsa wopha munthuyo mʼmanja mwa wobwezera magazi, ndipo amubwezere kumzinda wothawirako kumene anathawira. Iye ayenera kukhala mumzindamo mpaka mkulu wa ansembe amene anadzozedwa ndi mafuta opatulika adzamwalire.+
25 Kenako oweruzawo azipulumutsa wopha munthuyo mʼmanja mwa wobwezera magazi, ndipo amubwezere kumzinda wothawirako kumene anathawira. Iye ayenera kukhala mumzindamo mpaka mkulu wa ansembe amene anadzozedwa ndi mafuta opatulika adzamwalire.+