-
Numeri 35:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Komanso musamalandire dipo lowombolera munthu amene anathawira kumzinda wothawirako, nʼcholinga choti aloledwe kubwerera kwawo mkulu wa ansembe asanamwalire.
-