Deuteronomo 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa nthawi imeneyo ndinakuuzani kuti, ‘Sindikwanitsa ndekha kugwira ntchito yokutsogolerani.+