-
Deuteronomo 1:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndiyeno ndinakuuzani kuti, ‘Mwafika mʼdera lamapiri la Aamori, limene Yehova Mulungu wathu akufuna kutipatsa.
-