Deuteronomo 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Onani, Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli. Pitani, kalitengeni kuti likhale lanu, mogwirizana ndi zimene Yehova, Mulungu wa makolo anu anakuuzani.+ Musaope kapena kuchita mantha.’
21 Onani, Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli. Pitani, kalitengeni kuti likhale lanu, mogwirizana ndi zimene Yehova, Mulungu wa makolo anu anakuuzani.+ Musaope kapena kuchita mantha.’