28 Kodi tikupita kuti? Abale athu achititsa mantha mitima yathu+ potiuza kuti, “Kumeneko kuli anthu amphamvu zawo ndiponso ataliatali kuposa ifeyo ndipo mizinda yawo ndi ikuluikulu komanso ili ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba.+ Tinaonakonso ana a Anaki+ kumeneko.”’