Deuteronomo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pogwiritsa ntchito dzanja lake, Yehova anawachotsa pakati panu mpaka onse anatha.+