Deuteronomo 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tinalanda mizinda yonse yakudera lokwererapo, mʼGiliyadi monse, mʼBasana monse, mpaka ku Saleka ndi ku Edirei,+ mizinda imene inali mu ufumu wa Ogi ku Basana.
10 Tinalanda mizinda yonse yakudera lokwererapo, mʼGiliyadi monse, mʼBasana monse, mpaka ku Saleka ndi ku Edirei,+ mizinda imene inali mu ufumu wa Ogi ku Basana.