Deuteronomo 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Uike Yoswa+ kuti akhale mtsogoleri ndipo umulimbikitse ndi kumulimbitsa mtima chifukwa ndi amene adzawolotse+ anthuwa ndi kuwachititsa kulandira dziko limene ulionelo kukhala cholowa chawo.’
28 Uike Yoswa+ kuti akhale mtsogoleri ndipo umulimbikitse ndi kumulimbitsa mtima chifukwa ndi amene adzawolotse+ anthuwa ndi kuwachititsa kulandira dziko limene ulionelo kukhala cholowa chawo.’