-
Deuteronomo 6:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndipo inu Aisiraeli, muzimvetsera ndi kutsatira malangizo ndi malamulo akewo mosamala, kuti zinthu zikuyendereni bwino komanso kuti muchuluke kwambiri mʼdziko loyenda mkaka ndi uchi, mogwirizana ndi zimene Yehova, Mulungu wa makolo anu anakulonjezani.
-