Deuteronomo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 pothamangitsa adani anu onse mogwirizana ndi zimene Yehova analonjeza.+