Deuteronomo 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo tikamatsatira malamulo onsewa mosamala kwambiri pomvera* Yehova Mulungu wathu mogwirizana ndi zimene anatilamula, ndiye kuti tikuchita chilungamo pamaso pake.’”+
25 Ndipo tikamatsatira malamulo onsewa mosamala kwambiri pomvera* Yehova Mulungu wathu mogwirizana ndi zimene anatilamula, ndiye kuti tikuchita chilungamo pamaso pake.’”+