Deuteronomo 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sikuti Yehova anakusonyezani chikondi ndi kukusankhani+ chifukwa chakuti munali ochuluka kuposa mitundu yonse, chifukwatu mtundu wanu unali waungʼono mwa mitundu yonse.+
7 Sikuti Yehova anakusonyezani chikondi ndi kukusankhani+ chifukwa chakuti munali ochuluka kuposa mitundu yonse, chifukwatu mtundu wanu unali waungʼono mwa mitundu yonse.+