Deuteronomo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Muonetsetse kuti mukusunga lamulo lililonse limene ndikukupatsani lero, kuti mupitirize kukhala ndi moyo+ komanso kuti muchuluke, nʼkupita kukatenga dziko limene Yehova analumbira kwa makolo anu.+
8 “Muonetsetse kuti mukusunga lamulo lililonse limene ndikukupatsani lero, kuti mupitirize kukhala ndi moyo+ komanso kuti muchuluke, nʼkupita kukatenga dziko limene Yehova analumbira kwa makolo anu.+