Deuteronomo 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako ndinatembenuka nʼkutsika mʼphirimo pa nthawi imene phirilo linkayaka moto,+ ndipo miyala iwiri ya pangano inali mʼmanja mwanga.+
15 Kenako ndinatembenuka nʼkutsika mʼphirimo pa nthawi imene phirilo linkayaka moto,+ ndipo miyala iwiri ya pangano inali mʼmanja mwanga.+