Deuteronomo 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kutinso mukhale ndi moyo nthawi yaitali+ mʼdziko limene Yehova analumbira kwa makolo anu kuti adzawapatsa iwowo ndi mbadwa* zawo,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:9 Nsanja ya Olonda,8/1/2007, tsa. 29
9 kutinso mukhale ndi moyo nthawi yaitali+ mʼdziko limene Yehova analumbira kwa makolo anu kuti adzawapatsa iwowo ndi mbadwa* zawo,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi.+