Deuteronomo 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 kuti inuyo ndi ana anu mukhale ndi moyo wautali+ mʼdziko limene Yehova analumbira kwa makolo anu kuti adzawapatsa,+ kwa nthawi yonse imene thambo lidzakhale pamwamba pa dziko lapansi.
21 kuti inuyo ndi ana anu mukhale ndi moyo wautali+ mʼdziko limene Yehova analumbira kwa makolo anu kuti adzawapatsa,+ kwa nthawi yonse imene thambo lidzakhale pamwamba pa dziko lapansi.