Deuteronomo 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 muzikaonetsetsa kuti mukusunga malamulo ndi zigamulo zonse zimene ndikuika pamaso panu lero.”+