Deuteronomo 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova Mulungu wanu akadzawonjezera dziko lanu+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani,+ ndipo inu nʼkunena kuti, ‘Ndikufuna kudya nyama,’ chifukwa mukulakalaka kudya nyama, nthawi iliyonse imene mwalakalaka kudya nyama muzidzadya.+
20 Yehova Mulungu wanu akadzawonjezera dziko lanu+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani,+ ndipo inu nʼkunena kuti, ‘Ndikufuna kudya nyama,’ chifukwa mukulakalaka kudya nyama, nthawi iliyonse imene mwalakalaka kudya nyama muzidzadya.+