-
Deuteronomo 12:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Musamadye magazi, kuti zinthu zikuyendereni bwino inuyo ndi ana anu obwera mʼmbuyo mwanu, chifukwa choti mukuchita zinthu zoyenera pamaso pa Yehova.
-