-
Deuteronomo 12:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Popita kumalo amene Yehova adzasankhe, muzidzatenga zinthu zanu zokha zopatulika komanso zinthu zoti mukapereke nsembe pokwaniritsa lonjezo limene munachita.
-