Deuteronomo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Muzitsatira Yehova Mulungu wanu, muzimuopa, muzisunga malamulo ake, muzimvera mawu ake ndipo iye ndi amene muyenera kumutumikira komanso kumumamatira.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:4 Nsanja ya Olonda,10/15/2002, ptsa. 16-17
4 Muzitsatira Yehova Mulungu wanu, muzimuopa, muzisunga malamulo ake, muzimvera mawu ake ndipo iye ndi amene muyenera kumutumikira komanso kumumamatira.+