Deuteronomo 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Muzimuponya miyala kuti afe,+ chifukwa amafuna akuchotseni kwa Yehova Mulungu wanu, amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo, mʼnyumba yaukapolo.
10 Muzimuponya miyala kuti afe,+ chifukwa amafuna akuchotseni kwa Yehova Mulungu wanu, amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo, mʼnyumba yaukapolo.