Deuteronomo 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 muzipha ndithu anthu amumzindawo ndi lupanga.+ Muziwononga ndi lupanga mzindawo komanso chilichonse chimene chili mmenemo, kuphatikizapo ziweto zake.+
15 muzipha ndithu anthu amumzindawo ndi lupanga.+ Muziwononga ndi lupanga mzindawo komanso chilichonse chimene chili mmenemo, kuphatikizapo ziweto zake.+