-
Deuteronomo 13:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako muzisonkhanitsa zinthu zonse zimene mwapeza mumzindawo, pakati pa bwalo lake nʼkuwotcha mzindawo ndi moto. Ndipo zinthu zimene munapeza mumzindawo zidzakhala nsembe yopsereza yoperekedwa kwa Yehova Mulungu wanu. Mzindawo udzakhale bwinja mpaka kalekale ndipo usadzamangidwenso.
-