Deuteronomo 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho muzimvera* Yehova Mulungu wanu, posunga malamulo ake onse amene ndikukupatsani lero, mukatero mudzachita zinthu zoyenera pamaso pa Yehova Mulungu wanu.”+
18 Choncho muzimvera* Yehova Mulungu wanu, posunga malamulo ake onse amene ndikukupatsani lero, mukatero mudzachita zinthu zoyenera pamaso pa Yehova Mulungu wanu.”+