-
Deuteronomo 14:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 muzidzagulitsa chakhumicho ndipo muzidzatenga ndalamazo mʼmanja mwanu nʼkupita kumalo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe.
-