Deuteronomo 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndipo musaiwale Mlevi amene akukhala mumzinda wanu,+ chifukwa sanapatsidwe gawo kapena cholowa ngati inuyo.+
27 Ndipo musaiwale Mlevi amene akukhala mumzinda wanu,+ chifukwa sanapatsidwe gawo kapena cholowa ngati inuyo.+