Deuteronomo 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo musadzaimike chipilala chopatulika,+ chinthu chimene Yehova Mulungu wanu amadana nacho.”