Deuteronomo 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 muzitenga mwamuna kapena mkazi amene wachita chinthu choipayo nʼkupita naye kunja kwa mzinda, ndipo muzikamuponya miyala kuti afe.+
5 muzitenga mwamuna kapena mkazi amene wachita chinthu choipayo nʼkupita naye kunja kwa mzinda, ndipo muzikamuponya miyala kuti afe.+