Deuteronomo 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu onse adzamva zimenezo nʼkuchita mantha ndipo sadzachitanso zinthu modzikuza.+