-
Deuteronomo 17:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Akachita zimenezi sadzadzikweza pamaso pa abale ake, komanso sadzachoka pachilamulo nʼkupatukira kudzanja lamanja kapena lamanzere, kuti iyeyo ndi ana ake apitirize kukhala mafumu mu Isiraeli kwa nthawi yaitali.”
-